Yeremiya 43:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Nebukadirezara adzabwera kudzathira nkhondo dziko la Iguputo.+ Woyenera kufa ndi mliri adzafa ndi mliri. Woyenera kutengedwa kupita ku ukapolo adzatengedwa kupita ku ukapolo. Woyenera kufa ndi lupanga adzafa ndi lupanga.+ Ezekieli 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 “Uwauze kuti iweyo ndiwe chizindikiro cholosera zam’tsogolo+ kwa iwo. Zidzachitika kwa iwo monga mmene iwe wachitira. Iwo adzapita ku ukapolo, kudziko lina.+
11 Nebukadirezara adzabwera kudzathira nkhondo dziko la Iguputo.+ Woyenera kufa ndi mliri adzafa ndi mliri. Woyenera kutengedwa kupita ku ukapolo adzatengedwa kupita ku ukapolo. Woyenera kufa ndi lupanga adzafa ndi lupanga.+
11 “Uwauze kuti iweyo ndiwe chizindikiro cholosera zam’tsogolo+ kwa iwo. Zidzachitika kwa iwo monga mmene iwe wachitira. Iwo adzapita ku ukapolo, kudziko lina.+