Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 15:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ndiyeno akakufunsa kuti, ‘Tichoke kupita kuti?’ ukayankhe kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Woyenera kufa ndi mliri afe ndi mliri! Woyenera kufa ndi lupanga afe ndi lupanga! Woyenera kufa ndi njala yaikulu afe ndi njala yaikulu!+ Woyenera kutengedwa kupita ku ukapolo atengedwe kupita ku ukapolo!”’+

  • Yeremiya 20:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma kunena za iwe Pasuri, ndi onse okhala m’nyumba yako, mudzapita ku ukapolo.+ Iwe udzapita ku Babulo ndipo udzafera kumeneko ndi kuikidwa m’manda komweko pamodzi ndi anzako onse,+ chifukwa walosera kwa iwo monama.’”+

  • Yeremiya 44:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Yehova wanena kuti: “Ine ndikupereka Farao Hofira, mfumu ya Iguputo,+ m’manja mwa adani ake ndiponso m’manja mwa ofuna moyo wake,+ monga mmene ndinaperekera Zedekiya mfumu ya Yuda m’manja mwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo, mdani wa Zedekiyayo amene akufunanso moyo wake.”’”+

  • Yeremiya 52:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Anthu onyozeka pakati pa Ayudawo, anthu ena onse amene anatsala mumzindamo,+ anthu amene anathawira ku mbali ya mfumu ya Babulo ndi amisiri onse aluso, Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu, anawatenga kupita nawo ku ukapolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena