Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 14:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pamene akusala kudya ine sindikumvetsera kuchonderera kwawo.+ Pamene akupereka nsembe zopsereza zathunthu ndi nsembe zambewu ine sindikukondwera nazo,+ ndipo ndiwawononga ndi lupanga, njala yaikulu ndiponso mliri.”+

  • Ezekieli 5:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Gawo limodzi la magawo atatu a tsitsilo ulitenthe pamoto pakati pa mzindawo masiku ozungulira mzindawo akatha.+ Kenako utenge gawo lina la magawo atatuwo. Gawo limeneli uzilimenya ndi lupanga ukuzungulira mzinda wonsewo.+ Gawo lomaliza la magawo atatuwo uliuluze ndi mphepo ndipo ine ndidzalitsatira nditasolola lupanga.+

  • Zekariya 11:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Pambuyo pake ndinanena kuti: “Ndileka kukuwetani.+ Amene akufa, afe.+ Amene akuwonongeka, awonongeke. Otsalawo adyane.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena