Yeremiya 23:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “Anthu awa, aneneri, kapena ansembe akakufunsa kuti, ‘Kodi uthenga* wa Yehova ukuti chiyani?’+ uwayankhe kuti, ‘“Anthu inu ndinu katundu wolemetsa!+ Ndipo ndidzakusiyani,”+ watero Yehova.’ Zekariya 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Aterafi*+ amalankhula zoipa. Ochita zamaula amaona masomphenya onama+ ndipo amafotokoza maloto opanda pake. Iwo saphula kanthu polimbikitsa anthu.+ N’chifukwa chake adzasochere ngati nkhosa.+ Iwo adzavutika chifukwa adzakhala opanda m’busa.+
33 “Anthu awa, aneneri, kapena ansembe akakufunsa kuti, ‘Kodi uthenga* wa Yehova ukuti chiyani?’+ uwayankhe kuti, ‘“Anthu inu ndinu katundu wolemetsa!+ Ndipo ndidzakusiyani,”+ watero Yehova.’
2 Aterafi*+ amalankhula zoipa. Ochita zamaula amaona masomphenya onama+ ndipo amafotokoza maloto opanda pake. Iwo saphula kanthu polimbikitsa anthu.+ N’chifukwa chake adzasochere ngati nkhosa.+ Iwo adzavutika chifukwa adzakhala opanda m’busa.+