Yeremiya 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ndidzawachititsa kudya mnofu wa ana awo aamuna ndi ana awo aakazi. Aliyense adzadya mnzake, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene adani awo ndiponso anthu amene akufuna moyo wawo adzawapanikiza nazo.”’+ Ezekieli 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “‘“Choncho pakati pako, abambo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumphepo zonse zinayi.”’+
9 Ndidzawachititsa kudya mnofu wa ana awo aamuna ndi ana awo aakazi. Aliyense adzadya mnzake, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene adani awo ndiponso anthu amene akufuna moyo wawo adzawapanikiza nazo.”’+
10 “‘“Choncho pakati pako, abambo adzadya ana awo+ ndipo ana adzadya abambo awo. Ine ndidzakulanga ndipo anthu ako onse otsala ndidzawabalalitsira kumphepo zonse zinayi.”’+