53 Pamenepo udzadya chipatso cha mimba yako, mnofu wa ana ako aamuna ndi ana ako aakazi,+ amene Yehova Mulungu wako wakupatsa, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene adani ako adzakupanikiza nazo.
20 Munthu adzacheka kumbali yake yakumanja, koma adzakhala ndi njala. Adzadya kumanzere kwake, koma sadzakhuta.+ Aliyense adzadya mnofu wa dzanja lake.+