Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 26:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Chotero mudzadya ana anu aamuna ndi ana anu aakazi.+

  • Deuteronomo 28:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 kuti asagawireko aliyense wa iwo mnofu uliwonse wa ana ake aamuna amene adzawadya. Adzatero poona kuti alibiretu china chilichonse, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene mdani wanu adzakupanikizani nazo m’mizinda yanu yonse.+

  • Maliro 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Inu Yehova, yang’anani kuti muone+ yemwe mwamulanga chotere.

      Kodi amayi azidya zipatso za mimba yawo, ana awo athanzi?+

      Kapena kodi wansembe ndi mneneri aziphedwa m’malo opatulika a Yehova?+

  • Maliro 4:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Ngakhale mimbulu imapereka bere kwa ana ake kuti ayamwe.

      Koma mwana wamkazi wa anthu anga wakhala wankhanza+ ngati nthiwatiwa m’chipululu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena