Deuteronomo 28:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 ndipo sadzagawana nawo mnofu uliwonse wa ana ake aamuna amene adzawadye, popeza adzakhala alibiretu china chilichonse chifukwa cha mavuto oopsa amene mudzakumane nawo adani anu akadzazungulira mizinda yanu.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:55 Nsanja ya Olonda,8/1/1989, tsa. 29
55 ndipo sadzagawana nawo mnofu uliwonse wa ana ake aamuna amene adzawadye, popeza adzakhala alibiretu china chilichonse chifukwa cha mavuto oopsa amene mudzakumane nawo adani anu akadzazungulira mizinda yanu.+