Deuteronomo 28:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 kuti asagawireko aliyense wa iwo mnofu uliwonse wa ana ake aamuna amene adzawadya. Adzatero poona kuti alibiretu china chilichonse, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene mdani wanu adzakupanikizani nazo m’mizinda yanu yonse.+ Deuteronomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 28:55 Nsanja ya Olonda,8/1/1989, tsa. 29
55 kuti asagawireko aliyense wa iwo mnofu uliwonse wa ana ake aamuna amene adzawadya. Adzatero poona kuti alibiretu china chilichonse, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene mdani wanu adzakupanikizani nazo m’mizinda yanu yonse.+