Levitiko 26:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Chotero mudzadya ana anu aamuna ndi ana anu aakazi.+ Deuteronomo 28:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 kuti asagawireko aliyense wa iwo mnofu uliwonse wa ana ake aamuna amene adzawadya. Adzatero poona kuti alibiretu china chilichonse, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene mdani wanu adzakupanikizani nazo m’mizinda yanu yonse.+
55 kuti asagawireko aliyense wa iwo mnofu uliwonse wa ana ake aamuna amene adzawadya. Adzatero poona kuti alibiretu china chilichonse, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene mdani wanu adzakupanikizani nazo m’mizinda yanu yonse.+