Salimo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kodi ndidzalimbana ndi masautso anga kufikira liti?Kodi masiku a moyo wanga adzakhala odzaza ndi chisoni kufikira liti?Kodi mdani wanga adzadzikweza pamaso panga kufikira liti?+ Salimo 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Masautso a mtima wanga awonjezeka.+Ndilanditseni ku nkhawa zimene zili pa ine.+
2 Kodi ndidzalimbana ndi masautso anga kufikira liti?Kodi masiku a moyo wanga adzakhala odzaza ndi chisoni kufikira liti?Kodi mdani wanga adzadzikweza pamaso panga kufikira liti?+