Ekisodo 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo mkwiyo wanga udzakuyakirani,+ ndipo ndidzakuphani ndithu ndi lupanga, kuti akazi anu akhale akazi amasiye ndiponso ana anu akhale ana amasiye.+
24 Pamenepo mkwiyo wanga udzakuyakirani,+ ndipo ndidzakuphani ndithu ndi lupanga, kuti akazi anu akhale akazi amasiye ndiponso ana anu akhale ana amasiye.+