Salimo 109:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ana ake azingoyendayenda ndithu,+Ndipo azipemphapempha.Azichoka m’mabwinja mmene akukhala, n’kupita kukafunafuna chakudya.+ Yeremiya 11:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehova wa makamu wanena kuti: “Tsopano ndikuwapatsa chilango. Anyamata adzafa ndi lupanga.+ Ana awo aamuna ndi aakazi adzafa ndi njala yaikulu.+
10 Ana ake azingoyendayenda ndithu,+Ndipo azipemphapempha.Azichoka m’mabwinja mmene akukhala, n’kupita kukafunafuna chakudya.+
22 Yehova wa makamu wanena kuti: “Tsopano ndikuwapatsa chilango. Anyamata adzafa ndi lupanga.+ Ana awo aamuna ndi aakazi adzafa ndi njala yaikulu.+