Yeremiya 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero ana awo muwakhaulitse ndi njala yaikulu,+ ndipo aphedwe ndi lupanga.+ Akazi awo akhale amasiye ndipo ana a akaziwo afe.+ Amuna awo afe ndi mliri woopsa ndipo anyamata awo aphedwe ndi lupanga pa nkhondo.+
21 Chotero ana awo muwakhaulitse ndi njala yaikulu,+ ndipo aphedwe ndi lupanga.+ Akazi awo akhale amasiye ndipo ana a akaziwo afe.+ Amuna awo afe ndi mliri woopsa ndipo anyamata awo aphedwe ndi lupanga pa nkhondo.+