Salimo 50:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zindikirani zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.+ Aheberi 10:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma pali chiyembekezo china choopsa cha chiweruzo,+ ndiponso pali nsanje yoyaka moto imene idzawononge otsutsawo.+
22 Zindikirani zimenezi, anthu oiwala Mulungu inu,+Kuti ndisakukhadzulekhadzuleni popanda aliyense wokupulumutsani.+
27 Koma pali chiyembekezo china choopsa cha chiweruzo,+ ndiponso pali nsanje yoyaka moto imene idzawononge otsutsawo.+