Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 9:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Anthu oipa+ adzapita ku Manda,+

      Ngakhalenso anthu onse a mitundu ina amene aiwala Mulungu.+

  • Yesaya 51:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kodi n’chifukwa chiyani ukuiwala Yehova amene anakupanga,+ amene anatambasula kumwamba+ ndi kuyala maziko a dziko lapansi?+ N’chifukwa chiyani ukuchita mantha nthawi zonse, tsiku lonse lathunthu, poopa mkwiyo wa yemwe akukupanikizira mkati,+ ngati kuti iye wakonzeka kuti akuwononge?+ Kodi mkwiyo wa amene akukupanikizira mkati uli kuti?+

  • Yeremiya 2:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Kodi namwali angaiwale zodzikongoletsera? Kodi mkwatibwi angaiwale lamba wake wa pachifuwa? Koma anthu anga andiiwala kwa masiku osawerengeka.+

  • Hoseya 4:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Anthu anga adzawonongedwa chifukwa sakundidziwa.+ Popeza iwo akana kundidziwa,+ inenso ndidzawakana kuti azinditumikira ngati wansembe wanga.+ Popeza iwo aiwala lamulo la ine Mulungu wawo,+ inenso ndidzaiwala ana awo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena