Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 106:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iwo anaiwala Mulungu, Mpulumutsi wawo,+

      Amene anachita zinthu zazikulu ku Iguputo,+

  • Yesaya 17:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Popeza waiwala+ Mulungu wa chipulumutso chako,+ ndipo Thanthwe+ la chitetezo chako sunalikumbukire, n’chifukwa chake ukulima minda yokongola n’kumabzalamo mphukira ya mlendo.

  • Yeremiya 13:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Limeneli ndilo gawo lako, malo ako amene ndakuyezera,”+ watero Yehova, “chifukwa chakuti wandiiwala+ ndipo ukupitirizabe kukhulupirira zinthu zachinyengo.+

  • Yeremiya 18:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Pakuti anthu anga andiiwala+ moti amapereka nsembe zautsi kwa chinthu chopanda pake,+ ndiponso amapunthwitsa anthu amene akuyenda panjira zawo,+ m’njira zakale,+ ndi kuwayendetsa m’njira zina, njira zokumbikakumbika.

  • Hoseya 8:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Isiraeli anaiwala amene anamupanga+ ndipo anayamba kumanga akachisi.+ Yuda nayenso anachulukitsa mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+ Koma ine ndidzatumiza moto m’mizinda yake ndipo udzanyeketsa nsanja zokhalamo za mumzinda uliwonse.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena