Deuteronomo 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munaiwala Thanthwe limene linakuberekani,+Ndipo munayamba kuiwala Mulungu amene anachititsa kuti mukhalepo kudzera mwa zowawa za pobereka.+ Salimo 78:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Iwo sanakumbukire dzanja la Mulungu,+Sanakumbukire tsiku limene anawawombola kwa mdani wawo,+
18 Munaiwala Thanthwe limene linakuberekani,+Ndipo munayamba kuiwala Mulungu amene anachititsa kuti mukhalepo kudzera mwa zowawa za pobereka.+