Deuteronomo 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo ndinayamba kupembedzera+ Yehova ndi kunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu, amene ndiwo chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawawombola ndi mphamvu yanu, amene munawatulutsa mu Iguputo+ ndi dzanja lamphamvu.+ Salimo 78:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo anayambanso kuiwala zochita zake,+Ndi ntchito zake zodabwitsa zimene anawaonetsa.+
26 Pamenepo ndinayamba kupembedzera+ Yehova ndi kunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu, amene ndiwo chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawawombola ndi mphamvu yanu, amene munawatulutsa mu Iguputo+ ndi dzanja lamphamvu.+