Salimo 99:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+ Miyambo 15:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Yehova amakhala kutali ndi anthu oipa,+ koma amamva pemphero la anthu olungama.+ Yakobo 5:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+
6 Mose ndi Aroni anali pakati pa ansembe ake,+Samueli anali pakati pa anthu amene anali kuitana pa dzina lake.+Iwo anali kuitana Yehova, ndipo iye anali kuwayankha.+
16 Choncho muululirane machimo anu poyera+ ndi kupemphererana, kuti muchiritsidwe.+ Pembedzero la munthu wolungama limagwira ntchito mwamphamvu kwambiri.+