Salimo 34:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Maso a Yehova ali pa olungama,+Ndipo makutu ake amamva kufuula kwawo kopempha thandizo.+ Salimo 145:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndipo anthu amene amamuopa adzawachitira zokhumba zawo,+Adzamva kufuula kwawo kopempha thandizo ndipo adzawapulumutsa.+ Yesaya 58:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero inu mudzaitana ndipo Yehova adzakuyankhani. Mudzafuula popempha+ ndipo iye adzayankha kuti, ‘Ndikumva lankhulani!’ “Mukachotsa goli pakati panu,+ mukaleka kutosana chala+ ndi kulankhulana zopweteka,+ Yohane 9:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Tikudziwa kuti Mulungu samvetsera ochimwa,+ koma ngati munthu ali woopa Mulungu ndipo amachita chifuniro chake, ameneyo amamumvetsera.+
19 Ndipo anthu amene amamuopa adzawachitira zokhumba zawo,+Adzamva kufuula kwawo kopempha thandizo ndipo adzawapulumutsa.+
9 Chotero inu mudzaitana ndipo Yehova adzakuyankhani. Mudzafuula popempha+ ndipo iye adzayankha kuti, ‘Ndikumva lankhulani!’ “Mukachotsa goli pakati panu,+ mukaleka kutosana chala+ ndi kulankhulana zopweteka,+
31 Tikudziwa kuti Mulungu samvetsera ochimwa,+ koma ngati munthu ali woopa Mulungu ndipo amachita chifuniro chake, ameneyo amamumvetsera.+