Miyambo 6:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amatsinzinira ena ndi diso lake,+ amapanga zizindikiro ndi phazi lake, ndiponso amapanga zizindikiro ndi zala zake.+ Yesaya 57:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kodi mukusangalala chifukwa cha kuvutika kwa ndani?+ Kodi mukuyasamulira ndani pakamwa panu, ndi kum’tulutsira lilime?+ Kodi inu si inu ana a machimo, mbewu ya chinyengo,+
13 Amatsinzinira ena ndi diso lake,+ amapanga zizindikiro ndi phazi lake, ndiponso amapanga zizindikiro ndi zala zake.+
4 Kodi mukusangalala chifukwa cha kuvutika kwa ndani?+ Kodi mukuyasamulira ndani pakamwa panu, ndi kum’tulutsira lilime?+ Kodi inu si inu ana a machimo, mbewu ya chinyengo,+