Yesaya 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+ anthu olemedwa ndi zolakwa, mbewu yochita zoipa,+ ana obweretsa chiwonongeko.+ Iwo amusiya Yehova.+ Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu,+ ndipo abwerera m’mbuyo.+ Yesaya 30:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti amenewa ndi anthu opanduka,+ ana ochita zachinyengo,+ amene safuna kumva malamulo a Yehova,+
4 Tsoka kwa mtundu wochimwa,+ anthu olemedwa ndi zolakwa, mbewu yochita zoipa,+ ana obweretsa chiwonongeko.+ Iwo amusiya Yehova.+ Achitira Woyera wa Isiraeli zinthu zopanda ulemu,+ ndipo abwerera m’mbuyo.+
9 Pakuti amenewa ndi anthu opanduka,+ ana ochita zachinyengo,+ amene safuna kumva malamulo a Yehova,+