3 Izi zachitika chifukwa cha zinthu zoipa zimene mwachita ndi kundikhumudwitsa nazo. Mwafukiza nsembe zautsi+ ndi kutumikira milungu ina imene inu kapena makolo anu simunaidziwe.+
51 “Anthu okanika inu ndi osachita mdulidwe wa mumtima+ ndi m’makutu. Nthawi zonse mumatsutsana ndi mzimu woyera. Mmene anachitira makolo anu inunso mukuchita chimodzimodzi.+