Deuteronomo 9:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mwasonyeza khalidwe lopandukira Yehova+ kuyambira tsiku limene ndinakudziwani. Deuteronomo 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Choncho iye anati, ‘Ndiwabisire nkhope yanga,+Ndione kuti ziwathera bwanji.Pakuti iwo ndi m’badwo wokonda zoipa,+Ana osakhulupirika.+ Yoswa 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu aliyense wopandukira malamulo anu,+ ndi wosamvera mawu anu pa chilichonse chimene mungamulamule, ameneyo aphedwe.+ Inuyo mukhale wolimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.”+ Nehemiya 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+
20 Choncho iye anati, ‘Ndiwabisire nkhope yanga,+Ndione kuti ziwathera bwanji.Pakuti iwo ndi m’badwo wokonda zoipa,+Ana osakhulupirika.+
18 Munthu aliyense wopandukira malamulo anu,+ ndi wosamvera mawu anu pa chilichonse chimene mungamulamule, ameneyo aphedwe.+ Inuyo mukhale wolimba mtima ndipo muchite zinthu mwamphamvu.”+
26 “Koma iwo anakhala osamvera+ ndipo anakupandukirani.+ Anapitiriza kufulatira chilamulo chanu,+ ndipo anapha aneneri anu+ amene anali kuwalimbikitsa kuti abwerere kwa inu.+ Iwo anapitiriza kuchita zinthu zikuluzikulu zosakulemekezani.+