Deuteronomo 17:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Munthu amene adzadzikuza mwa kusamvera wansembe amene akutumikira Yehova Mulungu wako kapena mwa kusamvera woweruza,+ munthu ameneyo afe ndithu.+ Muzichotsa woipayo mu Isiraeli.+ 1 Samueli 11:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Tsopano anthuwo anayamba kuuza Samueli kuti: “Ndani akunena kuti, ‘Sauli sangakhale mfumu yathu?’+ Tipatseni anthu amenewo tiwaphe.”+
12 Munthu amene adzadzikuza mwa kusamvera wansembe amene akutumikira Yehova Mulungu wako kapena mwa kusamvera woweruza,+ munthu ameneyo afe ndithu.+ Muzichotsa woipayo mu Isiraeli.+
12 Tsopano anthuwo anayamba kuuza Samueli kuti: “Ndani akunena kuti, ‘Sauli sangakhale mfumu yathu?’+ Tipatseni anthu amenewo tiwaphe.”+