Miyambo 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Woipa akachotsedwa pamaso pa mfumu,+ mpando wake wachifumu udzakhazikitsidwa ndi chilungamo.+ Luka 19:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Komanso adani angawa, amene sanafune kuti ine ndikhale mfumu yawo, bwerani nawo kuno muwaphe ine ndikuona.’”+
27 Komanso adani angawa, amene sanafune kuti ine ndikhale mfumu yawo, bwerani nawo kuno muwaphe ine ndikuona.’”+