1 Mafumu 2:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Itatero, mfumuyo inalamula Benaya mwana wa Yehoyada amene ananyamuka n’kukakantha Simeyi, ndipo anafa.+ Choncho ufumuwo unakhazikika m’manja mwa Solomo.+ Esitere 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho anapachika Hamani pamtengo+ umene anakonzera Moredekai,+ ndipo mkwiyo wa mfumu unatha. Miyambo 20:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mfumu imakhala pampando wachiweruzo+ n’kubalalitsa zoipa zonse ndi maso ake.+
46 Itatero, mfumuyo inalamula Benaya mwana wa Yehoyada amene ananyamuka n’kukakantha Simeyi, ndipo anafa.+ Choncho ufumuwo unakhazikika m’manja mwa Solomo.+