Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 23:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Mulungu wa Isiraeli analankhula,

      Thanthwe la Isiraeli linandiuza kuti,+

      ‘Munthu wolamulira anthu akakhala wolungama,+

      N’kumalamulira moopa Mulungu,+

  • 1 Mafumu 2:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Solomo anakhala pampando wachifumu wa Davide bambo ake,+ ndipo m’kupita kwa nthawi, ufumu wake unakhazikika.+

  • 1 Mafumu 7:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Anamanganso Bwalo la Mpando Wachifumu,+ kumene anali kuweruzirako milandu. Bwaloli linkatchedwanso bwalo loweruzira.+ Makoma ake anali a matabwa a mkungudza kuchokera pansi mpaka kudenga.+

  • Mateyu 19:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Yesu anawayankha kuti: “Ndithu ndikukuuzani, Pa nthawi ya kulenganso zinthu, pamene Mwana wa munthu adzakhala pampando wachifumu waulemerero, inu amene mwatsatira ine mudzakhalanso m’mipando yachifumu 12, kuweruza mafuko 12 a Isiraeli.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena