Deuteronomo 32:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+ Salimo 144:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 144 Atamandike Yehova Thanthwe langa,+Amene akuphunzitsa manja anga kumenya nkhondo,+Amenenso akuphunzitsa zala zanga kumenyana ndi adani anga.
4 Iye ndi Thanthwe, ndipo ntchito yake ndi yangwiro,+Njira zake zonse ndi zolungama.+Mulungu wokhulupirika,+ amene sachita chosalungama.+Iye ndi wolungama ndi wowongoka.+
144 Atamandike Yehova Thanthwe langa,+Amene akuphunzitsa manja anga kumenya nkhondo,+Amenenso akuphunzitsa zala zanga kumenyana ndi adani anga.