1 Mafumu 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano usangomusiya, um’lange,+ poti ndiwe munthu wanzeru+ ndipo ukudziwa bwino zimene uyenera kumuchita. Utsitsire imvi zake+ ku Manda zili ndi magazi.”+ 1 Mafumu 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nthawi yomweyo Mfumu Solomo inatumiza lamulo kudzera mwa Benaya+ mwana wa Yehoyada. Iye anapita kukakantha Adoniya, n’kumupha.+ 1 Mafumu 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Kenako Benaya mwana wa Yehoyada anapita+ kuchihemako n’kukakantha Yowabu ndi kumupha,+ ndipo anaikidwa m’manda panyumba pake m’chipululu.
9 Tsopano usangomusiya, um’lange,+ poti ndiwe munthu wanzeru+ ndipo ukudziwa bwino zimene uyenera kumuchita. Utsitsire imvi zake+ ku Manda zili ndi magazi.”+
25 Nthawi yomweyo Mfumu Solomo inatumiza lamulo kudzera mwa Benaya+ mwana wa Yehoyada. Iye anapita kukakantha Adoniya, n’kumupha.+
34 Kenako Benaya mwana wa Yehoyada anapita+ kuchihemako n’kukakantha Yowabu ndi kumupha,+ ndipo anaikidwa m’manda panyumba pake m’chipululu.