1 Mafumu 2:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Nkhaniyo inam’fika Yowabu,+ ndipo iye anathawira kuchihema+ cha Yehova n’kukagwira nyanga za guwa lansembe.+ Paja Yowabu ankatsatira Adoniya,+ ngakhale kuti sanatsatire+ Abisalomu. 1 Mbiri 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma pa nthawiyo, chihema chopatulika cha Yehova chimene Mose anapanga m’chipululu ndi guwa lansembe zopsereza, zinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni.+
28 Nkhaniyo inam’fika Yowabu,+ ndipo iye anathawira kuchihema+ cha Yehova n’kukagwira nyanga za guwa lansembe.+ Paja Yowabu ankatsatira Adoniya,+ ngakhale kuti sanatsatire+ Abisalomu.
29 Koma pa nthawiyo, chihema chopatulika cha Yehova chimene Mose anapanga m’chipululu ndi guwa lansembe zopsereza, zinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni.+