1 Mafumu 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Chotero mfumu inapita ku Gibeoni+ kukapereka nsembe, chifukwa kumeneko ndiye kunali malo okwezeka ofunika kwambiri.+ Kumeneko, Solomo anapereka nsembe zopsereza zokwana 1,000 paguwa lansembe.+ 1 Mbiri 16:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anasiyanso Zadoki+ wansembe ndi abale ake ansembe kuchihema cha Yehova chimene chinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni,+ 2 Mbiri 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Solomo ndi mpingo wonsewo anapitira limodzi kumalo okwezeka a ku Gibeoni.+ Anapita kumeneko chifukwa ndi kumene kunali chihema chokumanako+ cha Mulungu woona, chimene Mose mtumiki+ wa Yehova anapanga m’chipululu.
4 Chotero mfumu inapita ku Gibeoni+ kukapereka nsembe, chifukwa kumeneko ndiye kunali malo okwezeka ofunika kwambiri.+ Kumeneko, Solomo anapereka nsembe zopsereza zokwana 1,000 paguwa lansembe.+
39 Anasiyanso Zadoki+ wansembe ndi abale ake ansembe kuchihema cha Yehova chimene chinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni,+
3 Kenako Solomo ndi mpingo wonsewo anapitira limodzi kumalo okwezeka a ku Gibeoni.+ Anapita kumeneko chifukwa ndi kumene kunali chihema chokumanako+ cha Mulungu woona, chimene Mose mtumiki+ wa Yehova anapanga m’chipululu.