1 Mbiri 16:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anasiyanso Zadoki+ wansembe ndi abale ake ansembe kuchihema cha Yehova chimene chinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni,+ 1 Mbiri 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Koma pa nthawiyo, chihema chopatulika cha Yehova chimene Mose anapanga m’chipululu ndi guwa lansembe zopsereza, zinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni.+
39 Anasiyanso Zadoki+ wansembe ndi abale ake ansembe kuchihema cha Yehova chimene chinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni,+
29 Koma pa nthawiyo, chihema chopatulika cha Yehova chimene Mose anapanga m’chipululu ndi guwa lansembe zopsereza, zinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni.+