1 Mbiri 21:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pa nthawiyo, chihema chopatulika cha Yehova chimene Mose anapanga mʼchipululu ndiponso guwa lansembe zopsereza, zinali pamalo okwezeka a ku Gibiyoni.+
29 Pa nthawiyo, chihema chopatulika cha Yehova chimene Mose anapanga mʼchipululu ndiponso guwa lansembe zopsereza, zinali pamalo okwezeka a ku Gibiyoni.+