Yoswa 9:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anthu a ku Gibeoni+ anamva zimene Yoswa anachita ku Yeriko+ ndi Ai.+ 1 Mafumu 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova anaonekera kwa iye kachiwiri, mofanana ndi momwe anamuonekera ku Gibeoni.+