Yoswa 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Adoni-zedeki anachita mantha kwambiri+ chifukwa Gibeoni unali mzinda waukulu ngati mzinda wolamulidwa ndi mfumu. Komanso mzindawo unali waukulu kuposa mzinda wa Ai,+ ndiponso amuna onse a kumeneko anali amphamvu. Yoswa 11:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Panalibe mzinda winanso umene unapangana za mtendere ndi ana a Isiraeli kupatulapo Ahivi+ okhala mumzinda wa Gibeoni.+ Ana a Isiraeli analanda mizinda ina yonse mwankhondo.+
2 Adoni-zedeki anachita mantha kwambiri+ chifukwa Gibeoni unali mzinda waukulu ngati mzinda wolamulidwa ndi mfumu. Komanso mzindawo unali waukulu kuposa mzinda wa Ai,+ ndiponso amuna onse a kumeneko anali amphamvu.
19 Panalibe mzinda winanso umene unapangana za mtendere ndi ana a Isiraeli kupatulapo Ahivi+ okhala mumzinda wa Gibeoni.+ Ana a Isiraeli analanda mizinda ina yonse mwankhondo.+