1 Mafumu 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ku Gibeoniko, Yehova Mulungu anaonekera+ kwa Solomo m’maloto+ usiku ndipo anati: “Pempha chimene ukufuna kuti ndikupatse.”+ 1 Mafumu 11:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma Yehova anamukwiyira kwambiri+ Solomo chifukwa mtima wake unapatuka kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ amene anamuonekera kawiri konse.+
5 Ku Gibeoniko, Yehova Mulungu anaonekera+ kwa Solomo m’maloto+ usiku ndipo anati: “Pempha chimene ukufuna kuti ndikupatse.”+
9 Koma Yehova anamukwiyira kwambiri+ Solomo chifukwa mtima wake unapatuka kwa Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ amene anamuonekera kawiri konse.+