1 Mafumu 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova anaonekera kwa iye kachiwiri, mofanana ndi momwe anamuonekera ku Gibeoni.+ 2 Mbiri 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Solomo ndi mpingo wonsewo anapitira limodzi kumalo okwezeka a ku Gibeoni.+ Anapita kumeneko chifukwa ndi kumene kunali chihema chokumanako+ cha Mulungu woona, chimene Mose mtumiki+ wa Yehova anapanga m’chipululu.
3 Kenako Solomo ndi mpingo wonsewo anapitira limodzi kumalo okwezeka a ku Gibeoni.+ Anapita kumeneko chifukwa ndi kumene kunali chihema chokumanako+ cha Mulungu woona, chimene Mose mtumiki+ wa Yehova anapanga m’chipululu.