Ekisodo 40:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Mwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo,+ udzautse chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako.+ Levitiko 1:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 1 Tsopano kuchokera m’chihema chokumanako,+ Yehova anaitana Mose ndi kulankhula naye kuti:
2 “Mwezi woyamba, pa tsiku loyamba la mweziwo,+ udzautse chihema chopatulika, kapena kuti chihema chokumanako.+