1 Mafumu 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ku Gibeoniko, Yehova Mulungu anaonekera+ kwa Solomo m’maloto+ usiku ndipo anati: “Pempha chimene ukufuna kuti ndikupatse.”+ 1 Mafumu 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova anaonekera kwa iye kachiwiri, mofanana ndi momwe anamuonekera ku Gibeoni.+
5 Ku Gibeoniko, Yehova Mulungu anaonekera+ kwa Solomo m’maloto+ usiku ndipo anati: “Pempha chimene ukufuna kuti ndikupatse.”+