2 Mbiri 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Usiku wa tsiku limenelo, Mulungu anaonekera kwa Solomo ndi kumuuza kuti: “Tandiuza, ukufuna ndikupatse chiyani?”+
7 Usiku wa tsiku limenelo, Mulungu anaonekera kwa Solomo ndi kumuuza kuti: “Tandiuza, ukufuna ndikupatse chiyani?”+