2 Mbiri 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndiyeno kumeneko Solomo anapereka nsembe pamaso pa Yehova paguwa lansembe lamkuwalo limene linali kuchihema chokumanako. Iye anapereka nsembe zopsereza 1,000 paguwalo.+
6 Ndiyeno kumeneko Solomo anapereka nsembe pamaso pa Yehova paguwa lansembe lamkuwalo limene linali kuchihema chokumanako. Iye anapereka nsembe zopsereza 1,000 paguwalo.+