1 Mafumu 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Nthawi yomweyo Mfumu Solomo inatumiza lamulo kudzera mwa Benaya+ mwana wa Yehoyada. Iye anapita kukakantha Adoniya, n’kumupha.+ Salimo 37:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Koma anthu onse ochimwa adzafafanizidwa.+M’tsogolo, anthu oipa adzaphedwa.+ Mlaliki 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Mulungu woona adzaweruza ntchito iliyonse ndiponso chinthu chilichonse chobisika, kuti aone ngati zili zabwino kapena zoipa.+
25 Nthawi yomweyo Mfumu Solomo inatumiza lamulo kudzera mwa Benaya+ mwana wa Yehoyada. Iye anapita kukakantha Adoniya, n’kumupha.+
14 Pakuti Mulungu woona adzaweruza ntchito iliyonse ndiponso chinthu chilichonse chobisika, kuti aone ngati zili zabwino kapena zoipa.+