2 Samueli 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Benaya+ mwana wa Yehoyada anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti.+ Ana aamuna a Davide anakhala ansembe.*+ 1 Mafumu 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Koma wansembe Zadoki,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, mneneri Natani,+ Simeyi,+ Reyi, ndi amuna amphamvu+ a Davide, sanagwirizane+ ndi Adoniya. 1 Mbiri 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mtsogoleri wa gulu lachitatu, lotumikira mwezi wachitatu, anali Benaya+ mwana wa Yehoyada+ wansembe wamkulu. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
18 Benaya+ mwana wa Yehoyada anali mtsogoleri wa Akereti+ ndi Apeleti.+ Ana aamuna a Davide anakhala ansembe.*+
8 Koma wansembe Zadoki,+ Benaya+ mwana wa Yehoyada, mneneri Natani,+ Simeyi,+ Reyi, ndi amuna amphamvu+ a Davide, sanagwirizane+ ndi Adoniya.
5 Mtsogoleri wa gulu lachitatu, lotumikira mwezi wachitatu, anali Benaya+ mwana wa Yehoyada+ wansembe wamkulu. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.