2 Samueli 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Yowabu anali mtsogoleri wa gulu lonse lankhondo+ la Isiraeli. Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali kutsogolera Akereti+ ndi Apeleti.+ 1 Mbiri 27:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mtsogoleri wa gulu lachitatu, lotumikira mwezi wachitatu, anali Benaya+ mwana wa Yehoyada+ wansembe wamkulu. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.
23 Yowabu anali mtsogoleri wa gulu lonse lankhondo+ la Isiraeli. Benaya+ mwana wa Yehoyada+ anali kutsogolera Akereti+ ndi Apeleti.+
5 Mtsogoleri wa gulu lachitatu, lotumikira mwezi wachitatu, anali Benaya+ mwana wa Yehoyada+ wansembe wamkulu. Gulu lake linali ndi anthu 24,000.