2 Samueli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika. 2 Samueli 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amasa mumuuze kuti,+ ‘Kodi iwe sindiwe fupa langa ndi mnofu wanga? Mulungu andilange mowirikiza+ ngati sudzakhala mtsogoleri wa gulu langa lankhondo nthawi zonse m’malo mwa Yowabu.’”+ 1 Mbiri 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yowabu mwana wa Zeruya anali mkulu wa gulu lankhondo,+ ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.
16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.
13 Amasa mumuuze kuti,+ ‘Kodi iwe sindiwe fupa langa ndi mnofu wanga? Mulungu andilange mowirikiza+ ngati sudzakhala mtsogoleri wa gulu langa lankhondo nthawi zonse m’malo mwa Yowabu.’”+
15 Yowabu mwana wa Zeruya anali mkulu wa gulu lankhondo,+ ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.