2 Samueli 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika. 1 Mbiri 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Chotero Davide anati: “Aliyense amene ayambirire kuukira+ Ayebusi akhala mtsogoleri ndiponso kalonga.” Pamenepo Yowabu+ mwana wa Zeruya ndiye anayamba kupita, choncho anakhala mtsogoleri.
16 Yowabu+ mwana wa Zeruya anali mkulu wa asilikali, ndipo Yehosafati+ mwana wa Ahiludi anali wolemba zochitika.
6 Chotero Davide anati: “Aliyense amene ayambirire kuukira+ Ayebusi akhala mtsogoleri ndiponso kalonga.” Pamenepo Yowabu+ mwana wa Zeruya ndiye anayamba kupita, choncho anakhala mtsogoleri.