Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yoswa 15:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Kenako Kalebe anati: “Aliyense amene agonjetse mzinda wa Kiriyati-seferi n’kuulanda, ndithu ndim’patsa mwana wanga Akisa,+ kuti akhale mkazi wake.”

  • 1 Samueli 17:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pamenepo amuna a Isiraeli anayamba kunena kuti: “Mukumuona mwamuna amene akubwerayu? Iye akubwera kudzatonza+ Isiraeli. Munthu amene angamukanthe ndi kumupha, mfumu idzam’patsa chuma chochuluka ndi kum’patsanso mwana wake wamkazi.+ Komanso, mfumu idzamasula nyumba ya bambo ake a munthuyo kuti isamapereke chilichonse mwa zinthu zimene Aisiraeli ayenera kupereka kwa mfumu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena