Oweruza 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndipo Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ mng’ono wake wa Kalebe, analanda mzindawo.+ Choncho, Kalebe anam’patsa Akisa mwana wake kuti akhale mkazi wake.+
13 Ndipo Otiniyeli+ mwana wa Kenazi,+ mng’ono wake wa Kalebe, analanda mzindawo.+ Choncho, Kalebe anam’patsa Akisa mwana wake kuti akhale mkazi wake.+